@iam_samjuma Komaso i donβt understand why you would roll your windows down nthawi ngati zimenezo and kudusaso malo ngati amenewo
AC mmagalimoto ndi ya ntchito yanji kodi?
Nde anzakewo akuchita kumveka kuti mu ntima angoti wadyapo
@I_Am_The_ICT Here in Malawi π²πΌ things are not stable, thereβs no forex, business are depending on black market dollar rates, inflation is has been high for years now