Spe : thako, lanjanja, ine mantha, ubwere pa room, mix ndasanja, plus ma zaza, homie ati wabanda, zandiphwanya, ku toilet ndaiwala tissue, sindiseka kwambili mix magwelu koma zandibanda
Goat : B Nyamula chikwama
@Punworld2 Akati Trapstar ndi chani Mesa ndi lifestyle ??? Ku poster BNB Kugona Bedsitter ๐๐๐๐๐๐ฝ
Beamer ya Atu ma spare parts agulidwe osamanamiza Anthu. ๐ซข๐ฅฒ
Kuyimba kundivuta bwanji ndisanayambe , Oyimba bwino anuwo alibe choti angaloze Ine si yes man a Nele inu ndi a dciik rider.
@MrDnD353868@tiidrotafrikka2 Kwanu konko ndi Trapstar wanu wamu bed sitter onyela chimbudzi chapanja yo Palibe mungandiuuze ine kaoneni pogona pa dolo wanuyo bloody shit.
@Siwinda_Jnr Komanso trapper wawo wakwa chinsapoyu alulowa chimbudzi cha panja nde aaaah Palibe chotutumutsa vuto lake mumangowaona PA internet anthuwa.