New update coming
WhatsApp akupanga zoti anthu tidzigwiltsa ntchito ma username basi ma phone numbers asamaoneke.
Izi zutanthauza kuti even mma group mu tidzingoonana ma username ngati pa Facebook or TikTok, koma phone number yamunthu sitidziionanso. Nginiyi pompano aipanga