Umugulire six pack ya brutal nde akuthaweso akamaliza kumwa, udziwe kuti wabesa 12 litres ya fuel pamenepo plus ubunyula basi.
Chisankho ndi chako bwanawe.
Apa azikazi odziwa what Valentines mean, akusakasaka zowagulira a boyfriend awo, nde Pali iweyo, matako ulibe, Koma ukudikira winawake azakubweletsere chocolate.Udya tuvi chaka chino galu iwe.🤣