#Times360Malawi
Mtsogoleri wa dziko lino, Professor Arthur Peter Mutharika, wati mavuto ena omwe dziko lino likukumana nawo ndi ochita kukonzedwa ndi anthu ena (man made problems pa chingerezi).
@TheLunaticGuy27@Itszingsmart Kuvutikaso kwachani iwe gadabwali? Zinthu zayamba kulongosoka apapa .....btw 3 million plus people voted that granny in power knowing full well that he old 🥱 so don't tell us what we already know 😉