🚨��🇸🇮🇷 #BreakingNews
Purezidenti Donald Trump polankhula za Iran:
“Sindingagwiritse ntchito zida za nyukiliya pomenyana ndi Iran. Sitikufunika kutero.
Bomba la Mother of All Bombs (MOAB) si bomba la nyukiliya.”
#Trump #Iran #USA #BreakingNews #MilitaryNews #MiddleEast
Ada awa ali ndi Zaka 70 anabwera kuno ku Malawi mu 1949 anabwera omasula masula monga momwe amapangila njinga zamoto Ada awa ayamba kugwira ntchito mu 1951 mpaka pano agwirabe ntchito ndipo ILALA imawaziwa mavuto amalawi
Nkhulukuta nyanja ambri akutelo♥️🇲🇼