Malawi music industry siinafikepo; ikadali poyesera zinthu, makamaka za ma show. Nanga show yomwe munthu ukuyembekezera anthu oposa 20,000, kenako n'kuika anthu 4 okha opanga ma scan a matikiti pa gate, achitetezo ochepa, aliyense kungovala za security koma osakhala mu team, .