Amuna Misso TV, a Malawian content creator known for his comedy and social commentary, has received a YouTube Silver Award after hitting 100K subscribers for his channel AM TV Malawi. ππ²πΌ
Apapa ndangoomuza friend ase tandijambuleko pafupi ndi mwala uwuwu wina akangondinena apapa ndiutole ndi mugende sinanga apapa ndayamba kumwa mikaka manaki naki kuti ndizitolerebe basi sinanga mukudziwa kale kuja nali kuja mkumadzi eti ndiye kumakhala kuthemula osati zibwana. Apapa tindevu tikubwelera and ka looks kajaso kayambaposo nde basi Amuna Misso Tv ibweleraso bhobho ββπ