Home
Language
English
Tรผrkรงe
Bahasa Indonesia
About
Privacy Policy
Terms of Service
Pricing
Sign In
Download All
Share
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
Father,slides ,shoes plug silver strickers fan๐ฉต๐ค , manchester united fan๐ฉตโค Football Analyst ๐ฒ๐ผMusic Analyst ๐,music or business promo Hit
Malawi Lilongwe
Joined May 2026
600
Following
119
Followers
203
Posts
ย Pinned Tweet
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
11 days ago
Ndaphunzira chinachake m'moyo uno koma sindingakuuzeni wina aliyense aphunzire yekha yekha.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
about 3 hours ago
Ndikati lelo sindikuufuna ndinama.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
about 17 hours ago
Zafika poti akabaza akandiona akumayilizilatu.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
about 23 hours ago
People would like to help you koma vuto mukutchena kwambiri.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
1 day ago
Ku old Age ku tigwira nazo murder kwachuluka ma temper.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
1 day ago
Chibwezi changoyamba dzulo,lelo massage ati "bebe Ana ako 4 Onse akhonza mayeso" ndangoti ah ah.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Mwinatu Road to success ija anayichosa window ndi khomo.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Mkazi aliyese amafuna mamuna wandalama. koma Pali akazi ena akuyenera kukumana ndifeo nanga mutani?
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Ziwachosani manyazi makolo anuwo. Anga alibwinobwino alibe manyazi.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Zipezereni mkazi opemphera ,osati basi akangomva phuu! Padenga aziti simundikwanisa
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Vuto umafuna ndizikukondani kuposa phone yanga.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Ingondiyezani malungo koma mukachuluka dzelu ndikasiya ka bukuka.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Ati ndalola koma sex ayi.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
2 days ago
Utha kumayesa ngati tonse tikuchimwatu ,osaziwa anzako akulapa each and every day.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Anzako akamasangalala umangoona ngati ndolowerela.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Chabwino muzingotinena mabodzawo koma musatiloze.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Poyamba makolo akayesa ngati ndikwatira mwansanga ,pano akuchita kudabwaso kuti koma akwatira ameneyu.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Zafikapa ndufunika m'bale wanga wakunja ndizimupangila ma projects ake.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Pena zoti wakula muziwira minbus ,umangomva tauzeni abambowo asuthe.
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Dziko la mkaka ndi uchi ( tsiru).
Mphatso Gogoda
@Amwenempha
3 days ago
Even moyowu si wathuso ,Athufe tilibiletu kathu.
Last Seen Users on Sotwe
Big Booty Babes 100K
Seen from
Turkey
Eathen436
Seen from
Pakistan
Tom Taylor Illustrated
Seen from
Portugal
Stephen
Seen from
Vietnam
Darkwolf
Seen from
Netherlands
Azgฤฑn ADAM ile eลinden gizli
Seen from
Turkey
ไบๅ็ถ
Seen from
United States
ูุญู ูู ูู ูู ูุฌุฑุงู
Seen from
Netherlands
Mohamed
Seen from
Australia
Rauw Gallego
Seen from
Spain
Trends for you
1
ariana
Under 10K tweets
2
#RaisingKanan
Under 10K tweets
3
Spain
Under 10K tweets
4
#petal
Under 10K tweets
5
Spider-Man
Under 10K tweets
6
Tom Holland
Under 10K tweets
7
RED Friday
Under 10K tweets
8
LIKE I DO
Under 10K tweets
9
Haley HOH
Under 10K tweets
10
Duran
Under 10K tweets
Most Popular Users
1
Elon Musk
@elonmusk
241.1M followers
2
Barack Obama
@barackobama
119.1M followers
3
Cristiano Ronaldo
@cristiano
112.4M followers
4
Donald J. Trump
@realdonaldtrump
111.8M followers
5
Narendra Modi
@narendramodi
107.1M followers
6
Rihanna
@rihanna
98.1M followers
7
NASA
@nasa
92.2M followers
8
Justin Bieber
@justinbieber
91.3M followers
9
KATY PERRY
@katyperry
88.7M followers
10
Taylor Swift
@taylorswift13
82.6M followers
11
Lady Gaga
@ladygaga
74.1M followers
12
Virat Kohli
@imvkohli
71.5M followers
13
Kim Kardashian
@kimkardashian
70.3M followers
14
YouTube
@youtube
68.7M followers
15
Bill Gates
@billgates
64.5M followers
16
Neymar Jr
@neymarjr
64.4M followers
17
The Ellen Show
@theellenshow
62.4M followers
18
CNN
@cnn
61.8M followers
19
Selena Gomez
@selenagomez
61.8M followers
20
X
@x
60.8M followers
Olivia
Online
โจ
โญ
๐ซ