Azibambo osamba inu malizeni amasai uyu size 10 only patseni ma 13 sau kutali i will send... Slippers yodyela nyama iyi gulani inu amuna akongolaπππππ
Ndiguleni ma slides awa boizi and gelozi 10pin yokha basi just name your size ndupezekela ku Lilongwe... Chabwino ngati simugula pangani retweet kuti ena onekoso ... Zikomo ππππ
When you meet him in heaven tell him his funeral was a celebration. That we danced to his songs. It was on live TV & BBC. Lilongwe was at stand still. There was a police escort. Don't find it arrogant when says, "ine ndi Martse ndi matha kuyimba ada"
Fare thee well Martse β£οΈ