mpamene nnakumbukila kut aaa mayendedwe aja siinali kuvuta kwanjinga koma kuti munthuyi sanathesese... komano imagine munthu kuziphuzsa wekha within a week then wautali panseu without any knowledge kuti panseu zimakhala motani.zufunika anthu ena ake achitepo kwathu
ine nkuti oky mukangopangisa service.. so tinagwirizana za go and back.. after nditatenga parcel ija tikubwerera anayamba kundiuza "njingayi ndagula 2 weeks ago" anatelo, ine nkuzati aaa zilibwino munalimbikila.. kenako nkuzati
"ndaziphunzisaso ndekha njingayi week yathayi"