@Lexaz_Lexaz Ife nde taona kuti Zilibwino kwambiri. Pricing ilinso bwinobwino. It's just business. The extra price is for the freedom of "kugula bundle motapitsa". After all ma options ndi ambiri. Ngati ena sakuziona bwino, choose other options🤣🤣🤣TNM ija yabwera 🔥 🔥
@WizbornX@JulioMulenga 🤣🤣zako zimenezo. Efelemu wanena wanena. Kwinako muona kuti mutani. Amene uja ndi shasha🤣simmamudziwa koma lero mwamudziwa. Ubwino wake wanenanso kale kuti ndiokhwima nde musamale🙌🤣
@WizbornX@JulioMulenga Zoti fixed wing airplane siingaime malo amodzi mmalere enafe timadziwa zimenezo pokhapokha ikhale yoti it was designed that way. Zilipo zina. But not dornier. Koma because of the effect yomwe ndikunenayo zimaoneka ngati choncho. Nkutheka he was in that condition koma sakudziwa.
@WizbornX@JulioMulenga Omwa Jada ndiiweyo. Simnanene kuti ndakhulupirira. Am saying kuti whether he is lying or not koma zoona ngati ndege yaima malo amodzi ndizotheka. It's called parallax effect. A simple Google search for you can go along way mmalo mongolemba ma accusations za ziiii.
@tiidrotafrikka2 These politicians don't understand the game. But then again they don't rate us all. They know they don't have to do sh*t. Just some t-shirt or bag of maize in 2030 then they r good. We let them abuse us. We don't demand enough from them.
@tiidrotafrikka2 🤣🤣🤣🤣🤣zadala izi. Aini akefe timangokhala. What do you expect?? Timafuna ena atimenyere nkhondo. Tiziatukwanaso in the process.
Parliament is trying to do its core function of oversight and somehow wina wakwiya eish🤣🤣the Judge was supposed to know better. Zovuta