@Kamoza0104 In 2015: ndinakanizidwapo then mokakamika adandilora kukhala,out 4 houses osakwatira ndidali ine mix padalitso asikana koma ayii ndithu,ndidakhalapo mpaka 3 years opanda kusokoneza banja olo mwana wamuthu. Bwenzi langa lidali TV ndi phone basi