@DzinkambaniJnr@widowakanda Ine andinenako kuwonda chochi simwa mwa ARV tanyozeka Ife koma mpaka kamangise munthu coz of wandinena sibwino saname ngti munthu ndiwe wamoyo umayenera kunenedwa ngti amanenedwa apresident iye ndani aaa inde zimawawa koma kukambirana thawi Zina kwabwino iye azalakwisa choposera