Koma mavuto ena timakumana nawo. Eish. Ndikumamfusa mulungu kuti anthu enawa munawalenga motani. Found out my neighbour has been using my mop, ndimangodabwa chikolopa chikumada modabwisa, yet when I'm done mopping it's clean cause I mop with soap. Told her akagule & she said no?