President wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika
Akuyembekezeleka kufika pa bwalo la kamuzu airtport masana Alero.
Mlembe wa mkulu wa President a Justin Saidi atsimikiza izi pa uthenga omwe watulutsidwa ku office yawo
Ambiri akumutana wanthuyi wavuta kwambiri ku Vietnam watinyamula molaro mkati, ndiye muli chi confidence, compassion, beauty that dazzles.
Malaw๐ฒ๐ผ to the World ๐!! Miss World!!
Kwathu kuno komwe bundle ili yotchipa kwambili kufanizira ndi maiko ena muno mu Africa โผ๏ธ
Kudos to MACRA Director General Dr Mayamiko Koloma.
Aseh wayamba bho keep it up ๐ฅ๐ฅ
Muthu sadzakhala ndimoyo ndi chakudya chokha koma kudya katatu ndikofunika lero akaidi amndende zamalawi akusimba lokoma pasi pa utsogoleri wa Professor Arthur Peter mutharika aka mkulukuta Moyo pomwe madyedwe asitha