Some time back people were travelin' mwaufulu apa yafika turn yathu ma airport atseka,Today I was supposed to fly to Dubai kotenga zinthu koma ai from nowhere ayambisa khondo 😑now I'm forced ku user road transport kuti ndikatengebe katunduyo moti apapa tili pa chingeni💔