@Kamoza0104 eh zina ukamva then you think about everything interest yose imathawa..why can't ladies stand on business these days abale...The guy friend naye ngofunika kumufinya ma balls zoba...Makhalidwe ake amanewa pamawa mamuna wa banja akamazasowa muzizamvesa chisoni...pa-ntu.....
@Kamoza0104 easy my gee hustle is slow these days..time time basi...amadyesa mbalame ase at the end of the day tidya...koma ngati sizitheka mpaka 7 halla tigawana komwe ndili nakoka...
@Kamoza0104 eh chonchi tikwatila?such a painful act...opusa ndi home boy yo cause kudya mkaz wapa banja is bad and risky cause eni kudziwa you gone gee