#TheDailytimes front page: Roads Fund Administration (RFA) says it has, for the past three years, been financing road maintenance works using revenue from toll gates after the Treasury stopped remitting fuel levy funds to the Roads Fund.
https://t.co/qOuRXtcuOQ
#Times360Malawi
Amalawi adzudzula mtsogoleri wa dziko lino, a Lazarus Chakwera, kaamba ka utsogoleri wosamvetsera mavuto awo.
Poyankhula mu nthawi ya Kulinji pa wailesi ya Times, anthu ku Dowa, Lilongwe, Kasungu, Balaka, Zomba, Neno komanso ku Mchinji, ati iwo adavotera