A friend athu angoyika kumene stethoscope pa rear view mirror, akuti akawaimitsa azingoti akuthamangila emergency kuchipatala,dzana sipholi inawaimisa coz some guy collapsed amafunika first Aid n they thought nd wachipatala,nde anaigwilatu ntchito, apapa maliro akuti nd onyamula
Tinali ku mowa... A friend sanadziwe zoti asemphanitsa ma Apple watch with his girlfriend pokamusiya. He just got a notification that her heart rate is at 150bpm and she's burnt 380 calories in 28 minutes.. Apa tupita komko.
Good Morning
Allow me to properly introduce myself
Karen Tadala Tembo
Bachelor of Science in Food Science and Technology (LUANAR, Malawi 🇲🇼)
Master of Science in Resource Utilization and Plant Nutrition (CAU, China 🇨🇳)
It’s two degrees hotter in here