@Sammymw01 @tendaimalata_ I second lol that's why tili ang'ono we were told n taught to be careful with our actions kuopesa pa mawa. Cz munthu zi ntchito zako zimakuikila umboni/ zimakulondola. It might happen it was a one time thing, koma anthu basi anamuika mugulu lakubalo
@EllenManda4 Ndi vinkhuwala in Zambia, one of my favorite 😋. zimakoma uzikazingile ndi tsabola, you will thank me later. Used to be one of the people disgusted by vinkhuwala masten akagula till I gave it a try naona kuti ndimachedwa. Would rather eat vinkhuwala than impwa