@Kauka_Af Koma zoti DNA yumafika 740k per child mukudziwa๐๐and these other hospitals ngat ku Adventist amafuna legal document oho ayi all the best ngat siwanu lerani chabe mwana wa nzako ndi wako yemwe๐๐๐คฃ๐
@JoramMD I was at Lilongwe girls secondary school and we had some Zimbabweans who thought were better than us in a NATIONAL GOVERNMENT school๐๐๐คฃ๐คฃ๐oho awa nde ndi too much kutiposa
@Lywellalufands Just a concerned nurse...anawa sore Ili pakamwapo muganizila allergy iliyose?or just a normal rash...atafunitseni albendazole and also try kusintha cooking oil all in all this is nice nafe next 5 years tipanga nawo