OIMBA AMBILI KU MALAWI KUNO SADZIWA KUPANGA NDALAMA NDI NYIMBO ZAWO BUT DEPEND ON SHOWS, HE'S RIGHT
ON THE OTHER HAND, ENA KAWADINYA PAKHOSI
PEOPLE LIKE TO TROLL CERTAIN ARTISTS KOMA ASANYOZE WAWOYI AYI, ANTHU ATSANKHO MULI PANO, NDE MUKULIRASO MOKWEZA HAHA BOMBOOO
Koma ma fans a spe ali ngati guru la alphabet aliese kufuna kumukakamiza kuti akonde spe, iyayi ma guy enafe timavera achina nkasa,gwaladi,skeffa chimoto, charles nsako and zabhobho