Happy Birthday, Mommy! โค๏ธ๐
Happy birthday to our beautiful spiritual mother, Prophetess Mary Bushiri! ๐น
Thank you for your love, wisdom, prayers, and spiritual covering. We thank God for the gift of your life and for the blessing of having you as our spiritual mother.
Pali anthu ochuluka amene mukadzamva mbiri yamoyo wawo mudzasiya kuwaweluza koma mudzayamba kuwapempherera. Anthu akudutsa munyengo zosiyanasiyana zoti mwina sangaziyankhule koma amangozintha kapangidwe ka zithu. Ena akupanga ma mistake chifukwa ali pansi pa pamvu ya mdani?
Ina si make up koma kuthawa angongole
Nkhope kutuwitsa kuchita kufanana ndi mbatatazo eeee๐๐คฃ
Munthu Ali barefoot chipangila makeup ndichani๐๐๐๐
APOLISI KU KARONGA AKUSAKASAKA BANJA LINA LOMWE LAPITA KU JONI , NDIKUSIYA MWANA WA DZAKA 40 YEAR'S YEKHA PAKHOMO.
๐ซฃ๐ซฃ๐ซฃ๐ซฃ๐คช๐คช๐คช๐คช๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ
David defeated Goliath but lost to the spirit of lust. The real giants are the desires you haven't killed.
Don't give in, Fight a good fight of faith & grow.
There is nobility in growth.
1 Corinthians 9:27 (kiv)
Luke 18:1
Psalm 91:7-9
A thousand may fall at your side, And ten thousand at your right hand; But it shall not come near you. Only with your eyes shall you look, And see the reward of the wicked. Because you have made the Lord, who is my refuge, Even the Most High, your dwelling place.
Koma a Malawi amatha kunyozaaaaa, yooo!! Ndagoma nanu!! Eh eh eh kkkkk, kunyoza tu kunyoza!!! Kaya, za #ekhonomy๐๐
(Anthu adaswana zedi ku Malawi. Ambiri alibe zochita koma basi kumangokhalira kukwiya, nkumanyoza. Kunyoza ndiye employment yawo.)
This morning, under the inspiration of the Holy Ghost, I prophesy to all God fearing and hard working souls in various fields, though your beginning might be small and despised, but the end will be great and shocking, for the Lord your God will take over until the task is well