@Mbirisale Nakhalako Malo achoncho was told kuti nkachifinya nzichisunga mnyumba ku kitchen or ku bafa basi chiziuma mnyumba momo..... Zinthu monga tsache, chikolopa mchere ndizoopsa kwambili kumapasana zimangovuta
@Hopemalopa Zimafunika usananyamuke mutsegule account in it name uzingoponyako ndalama kumeneko . Yachithandizo kumawatumizila ku ma account awo... Men trust us koma eeeeee kungomva Dubai uli iii apanga Zina my gender ๐๐๐ this is bad zisamafike apa