Top Tweets for #2025GeneralElection
#2025GeneralElection
Outgoing Vice President, Michael Usi, has conceded defeat in the presidential election, in which he contested under 'Okudya Zake Alibe Mlandu' party.

#2025GeneralElection
Mneneri wa bungwe la MEC a Sangwani Mwafulirwa wati wapampando wa bungweli Justice Annabel Mtalimanja alengeza zotsatira zachisankho madzulo ano osati 2 Koloko ngati mene analengezera poyamba.

#2025GeneralElection
The Human Rights Defenders Coalition (HRDC) has asked Malawians to embrace peace and unity as MCP President Lazarus Chakwera has conceded defeat to Professor Arthur Peter Mutharika of the Democratic Progressive Party (DPP).

#2025GeneralElection
Akuluakulu ena amukomiti yaikulu yachipani cha United Democratic Front (UDF) apereka mafuno abwino kwa m'tsogoleri wachipani cha Democratic Progressive (DPP), a Peter Mutharika ati kamba kotsogola pa chisankhochi.

#2025GeneralElection
Wapampando wabungwe la MEC Justice Annabel Mtalimanja wati akwanitsa kulandira zotsatira zachisankho kuchokera ku makhonsolo onse 36.

Malawi stands at a political crossroads once again, and the #2025generalelection has captured the attention of citizens, the region, and international observers. With results yet to be officially announced... https://t.co/5YfICypLsH

#2025GeneralElection
Malingana ndi bungungwe la MEC kufikira pano, 60.47 % ya anthu aponya voti.

#2025GeneralElection
Wapampando wa bungwe la MEC Justice Annabel Mtalimanja wati ntchito yoponya voti yomwe inayima pa malo oponyera voti a sukulu ya Mpata ku Nkolokoti, Ndirande (Matope constituency) yayambiranso ndipo itha 8 koloko usiku uno.

#2025GeneralElection
Pamene akulankhula ndi atolankhani, a Mtalimanaja apempha anthu omwe alibe ziphaso zovotera koma analembetsa kuti apitebe ku malo oponyera voti komwe akawathandize.
Iwo atsimikiza kuti anthuwa akakwanitsa kuponya voti.
#2025GeneralElection
Wapampando wa bungwe loona za chisankho la MEC Justice Annabel Mtalimanja wati ndondomeko yoponya voti mmalo onse 15,148 ikuyenda bwino.
Mwazina a Mtalimanja atsimikizanso kuti malo omwe anayamba kuponya voti mochedwa atsekanso kochedwerako.

#2025GeneralElection
Zonse zayamba bwino pamalo oponyera chisankho a Njedza ku m’mwera m'boma la Mulanje.
Pomwe nthawi imati 06:25 mmawa, anthu anali atayamba kuponya voti.
Malowa ali ndi anthu 2,033 omwe analembetsa kudzaponya voti.

#2025GeneralElection
Kuponya voti kunayamba mochedwa ndi mphindi pafupifupi 30 pa malo oponyela voti a Rumphi Catholic Primary School kaamba koti makina ena samagwira ntchito.

#2025GeneralElection
A Phunziro Mvula, omwe akuyima nawo pa chisankho ngati President, aponya voti yawo pa secondary school ya Dzenza mu constituency ya Lilongwe City Dzenza.

#2025generalelection
Anthu ochokera madera osiyanasiyana akukhamukira pa malo oponyera voti a Kalema ku m'mwera m'boma la Ntchisi.
Koma ngakhale izi zili chomwechi ntchitoyi sinayambe .

Honored to attend today's press briefing on tackling violence against women in elections by @OxfamMalawi
With the #2025GeneralElection approaching, let's continue the conversation to secure a gender transformative democracy free of violence in Malawi 💜

@UKUpdates_co_uk 2027? That's nowhere near early enough.....just think of how much more damage they could do to our country if we have to wait that long. Starmer's goose is cooked.....General Election now.
#2025GeneralElection
Kuelekea ;
#katibampya 🟰#Tanzaniampya
#2024localgovtelection
#2025generalelection
KATAVI!……Imetoa tamko!
@ChademaTz @ACT_wazalendo1 @ccm_tanzania
Last Seen Hashtags on Sotwe
minichat
Seen from Turkey
thisismurphyC
Seen from France
BlackedGeneration
Seen from Greece
三浦葵
Seen from United States
JonnysYellowSink
Seen from United States
花木槿のお茶会
Seen from United States
caregiving
Seen from Canada
public groping
Seen from Puerto Rico
レギオンリーグ
Seen from Vietnam
mk8D
Seen from Italy
Most Popular Users

Elon Musk 
@elonmusk
241.7M followers

Barack Obama 
@barackobama
119M followers

Cristiano Ronaldo 
@cristiano
114.6M followers

Donald J. Trump 
@realdonaldtrump
111.9M followers

Narendra Modi 
@narendramodi
107.2M followers

Rihanna 
@rihanna
98.7M followers

NASA 
@nasa
92.4M followers

Justin Bieber 
@justinbieber
91.8M followers

KATY PERRY 
@katyperry
90.1M followers

Taylor Swift 
@taylorswift13
84M followers

Lady Gaga 
@ladygaga
75.5M followers

Virat Kohli 
@imvkohli
73.5M followers

Kim Kardashian 
@kimkardashian
70.9M followers

YouTube 
@youtube
68.8M followers

Neymar Jr 
@neymarjr
66.5M followers

Bill Gates 
@billgates
65.2M followers

Selena Gomez 
@selenagomez
63.1M followers

The Ellen Show
@theellenshow
62.3M followers

CNN 
@cnn
61.8M followers

X 
@x
60.7M followers












