Top Tweets for #Mingoli
#Mingoli pa Chiwiri ili mkati ,kuswa sound zokhazokha zakumalawi, sankhani zomwe mmakonda tivine kunja kwazizira uku.
Whatsapp +265999952102
Calls +265884111025
#keepitcapital https://t.co/9qzrvRW6Zr via @FacebookWatch
Atoht Manje - Moyo #NowPlaying for the first time @CapitalFMMw. Imeneyi mukuimva bwanji mabwana?
#TuneIn. #Mingoli #Malawi
#NowPlaying Jolo Justice - Mimba ndi yanga @CapitalFMMw. #TuneIn... Nyimbo imeneyi mukuimva bwanji mabwana ndi madona?
#Mingoli
#Malawi
Tsopano DNA - Azasintha is #NowPlaying @CapitalFMMw mu #Mingoli. Kodi akulu amenewa aimba bwino kapena ayi?
#Malawi
#NowPlaying Grecium Nyambo - Ndidalira inu koyamba @CapitalFMMw. taiweluzeninso imeneyi omvera.
#Mingoli
#Malawi
The Daughters Band - Agama #NowPlaying @CapitalFMMw. Mukuimva bwanji mabwana ndi madona. #StayTuned
#Mingoli
#Malawi
Kebeh Tojef - Chikondi ndi awiri #NowPlaying @CapitalFMMw. #TuneIn and tiuzeni kuti mukuimva bwanji?
#Mingoli
#Malawi
#NowPlaying Evangelist - Safe for the first time @ @CapitalFMMw. #TuneIn munene maganizo anu mmene mukuimvelera nyimboyi.
#Mingoli
#Malawi
Lero omvera mwatibebetsera program @CapitalFMMw , zikomo. Ma Blacks mwachea nawo bwino kwambiiiiiiri. Mudzigona patali ndi moto.
#KeepItCapital #Mingoli
#Malawi

Tipatsaneko moni wa lolemba pa Capital FM pamene tikukumbutsana kale lathu kudzera munyimbo. Inuyo mwaswera bwanji kaya? @CapitalFMMw #Mingoli
#TuneIn
#Malawi
#NowPlaying Katelere Ching'oma & Moses Makawa @CapitalFMMw. Iyiyi mukuimva bwanji?
#TuneIn #Mingoli
#Malawi
The KHN Music #NowPlaying @CapitalFMMw, with a piece of music called African Lady. Mukuimvera bwanji omvera imeneyi? #TuneIn to #Mingoli
#MalawiUrbanMusic
Vijay - Mya Wife is #NowPlaying for the first time @CapitalFMMw. #TuneIn kuti nanunso mupange judge mmene mukuimvelera. #Mingoli
#Malawi #UrbanMusic
Hey! Let's meet @CapitalFMMw from 2:30PM up to 3:00PM kuti ticheze ndi Miracle Chinga. Muli ndi funso kapena ndemanga?
#Mingoli
#Malawi

#UrbanMingoliTop10 back on your radio! Please #TuneIn @CapitalFMMw and tatiuzeni mumafuna mu chart imeneyi mutakhala nyimbo yanji ya urban?
#Mingoli
#Malawi
Robert Piyo Dancy - Mwasemphana ndi madalitso #NowPlaying @CapitalFMMw for the first time. Imeneyi mukuimva bwanji omvera? #TuneIn
#Mingoli #Malawi
#NowPlaying Mtilatila ft DNA for the first time @CapitalFMMw. imeneyi nde mukuimva bwanji omvera? #TuneIn
#Mingoli #MalawiUrbanMusic
#NowPlaying Obiyo - Ndilore for the first time @CapitalFMMw.Tanenani omvera kuti imeneyi mukuimva bwanji? #TuneIn #Mingoli
#Mingoli
#Malawi
#NowPlaying Complete Onel - I need your love for the first time @CapitalFMMw. Tanenani omvera kuti imeneyi mukuimva bwanji? #Mingoli
#Malawi #UrbanMusic
Last Seen Hashtags on Sotwe
Most Popular Users

Elon Musk 
@elonmusk
241.7M followers

Barack Obama 
@barackobama
119M followers

Cristiano Ronaldo 
@cristiano
114.4M followers

Donald J. Trump 
@realdonaldtrump
111.9M followers

Narendra Modi 
@narendramodi
107.2M followers

Rihanna 
@rihanna
98.7M followers

NASA 
@nasa
92.4M followers

Justin Bieber 
@justinbieber
91.8M followers

KATY PERRY 
@katyperry
90M followers

Taylor Swift 
@taylorswift13
83.9M followers

Lady Gaga 
@ladygaga
75.4M followers

Virat Kohli 
@imvkohli
73.4M followers

Kim Kardashian 
@kimkardashian
70.9M followers

YouTube 
@youtube
68.8M followers

Neymar Jr 
@neymarjr
66.4M followers

Bill Gates 
@billgates
65.2M followers

Selena Gomez 
@selenagomez
63.1M followers

The Ellen Show
@theellenshow
62.3M followers

CNN 
@cnn
61.8M followers

X 
@x
60.7M followers


