@Madala_snnogah Kuyambila bobi ndi fada amawopa madness😂 fadamoti ndi label yake onse zikuwavutilapo Mu industry mu kuti nyimbo yawo ikhale ndi motion akudikila ayambane Kaye ndi madness💀
@JukeJamMw@_jouce Ngati atapite kushow akhala ngati kape chifukwa he won't get paid and akuyimba ulele Ku show ya hater. Imeneyo ndi ntchito ya kalavula gaga