Hi everyone. I have a story to share on behalf of someone who’s seeking advice.
A lady was engaged and living with her fiancé. One day, her fiancé’s sister reached out, asking if she could come live with them. Out of kindness and sympathy, the woman agreed and informed her fiancé
Bwana Tonderai Banda yemwe ndi Manager wa Onesimus komanso mwini wake wa Entertainers Promotion and Stake Out Lounges nawo akuoneka kuti amukonzera kenakake katswiriyu.
Ngati sichoncho mwina akufuna kumuthandiza kupititsa patsogolo talent yake munjira ina yapadera.
Seems Chippie Uwah achimaliza bwinotu chakachi!
After kulandira 1.2 million kwacha kuchokera kwa ma lady fans ake awiri from USA omwe akuti ngakhale Chippie sanawine award iliyonse ku MBC Entertainers Award 2024 koma iwowo amamufirabe...
Kabanja kodala! The Kingstons... Congratulations 👏
Chaka chatha kalechi...New Ambassadorship deal, New Car and a gift voucher of 5 million kwacha from GoFresh Ltd.
Happy birthday Noel Limbani Innocent Jack Juma Chikoleka-Banda.
Also known as Phyzix, Mountain GOAT, Don Gamba, Captain Bae, Man Phyzo, Gamba wa Suit, Orphan Boy, Atigo, Hip Hop, Cholapitsa.
Iye polemba pa tsamba lake la Facebook wamaliza nkuti "Soon South Africans will wake up to real agenda happening in their land- hating men of God and celebrating evil. Diabolica!"
#nyasaplug#feedthyfomo
Bushiri Vs Chris Brown.
Wadandaula Prophet Shepherd Bushiri ati indeed, if you hate someone, even your most beautiful face looks ugly.
Zonsenzitu zikudza pomwe anthu komanso ma media houses ambiri kuphatikizapo aku South Africa akumupopa Chris Brown kuti ndi Crowd Puller
chifukwa chodzadzitsa FNB Stadium ku South Africa yomwe capacity yake ndi 94,000 + people.
Bushiri akuti iyeyo anadzadzitsapo stadium yi ndi anthu 110,000 maulendo okwana 4 koma ma media houses a m'dzikolo sanalembe izi.
Police at Kamuzu International Airport in Lilongwe, Malawi, have today arrested 49-year-old South African woman, Funiwe Abigail Nkcosolwana for possession of cocaine.