@kaymartin_iv I can't agree coz ifeyo tinali ana nthawi ya real elements koma timamva kuti kunali ntchito osati masewera, I even checked out their video on YouTube eeeeeh kunali nkhondo koma if you are to choose your all time favourite ukamba za nthawi yomwe iwe umatsata
@kaymartin_iv 1st time I heard street fame's "Buns and hands" verse ya T1 made me feel like we were ready to export, the other side ya Leo ikuyenera kukhalaponso, same era Kuli Homegrown African. Mwachidule I think tili ndi nyimbo zambiri za hard koma were never export. Olo iweo ngwa bhonso 🤣
@kaymartin_iv Nde kuli yama 2010s ukukambayi, imeneyinso achina JB anazaipanilira ndi achina mkazi ogulugusha, sungamutole mafo akazi ndi mowa 🤣 sindimaiwalanso first time I heard "I do" by Jillz ndi Pricy coz their shid sounded like it was produced outside Mw, Viceroy's "Lethal" 🔥
@kaymartin_iv Young Kay's "exhale" and "first impression" albums, real elements nyambo tiye nazo, Tino's "kamu hood" era imene ija kunalinso nyimbo za hard
@kaymartin_iv To me singakhalepo imodzi koma that is one of them. Coz our industry imatengera kuti munthuwe umatsata kwambiri era iti. Pali ya ma 2000s ya achina Dynamike, Renegade, Pilgrim, Lomwe, Bomb squad, Ndabwera, Banyamulenge, kulimbana ndi njuchi, Ntofu ya Kenny Klips,