Koma generation imene inakula nthawi ya Kamuzu ndiyopanda mwambo. Inangozaza ndi anthu akuba, daily mu news bambo awinawake akumakhala kuti aba chuma chaboma penapake.
They are always busy criticizing the ama 90's and 2000's yet generation yawo inangozaza ndi anthu akuba.
@naferene_ Ine I'm so discontented with how they are aligning their offspring to eventually take over. 2030 is a make or break apo ayi we are in for another 3 decades of mediocrity.
@HystonKayange@Turnt_Lotus You begin to ask them directly such questions; they quickly become cry babies, talkn bout mukutipangila nsanje. Among them, some want to take up public positions btw, tizakhanzikana bwanji?