@PempheroMphande These big business pipo that are doing in our country they are tax invaders and apapa ndi game over that's why zonsezi akupangazi akudziwa kuti agwidwa pant down
The tax base ipanga zoti itutumikire ife amalawi, let's love dziko lathu, tisalole awa obwerawa atiwononge dzikoli.
@PempheroMphande Kungoti ambiri we're blind koma these lads they're misusing religious so called of peace, awawa sianthu abwino when it comes to hate it's a dirty trait.