@Taffie_1998 Choyamba ndipeleke moni.mwadzuka bwanji a Malawi? CU ndi university yabwino koma ndati koma kumapita mbuli.Ana oti kwawo kwangokhala makobili koma ali https://t.co/ez9Q4IgeLa points 50 koma chifukwa cha makobiliri amakwanitsa kutenga degree.Had it been amatenga based on merit bo